Matthew 21:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Yesu adaŵasiya, natuluka mumzindamo kupita ku Betaniya, nakagona kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anawasiya, natuluka m'mzinda, napita ku Betaniya, nagona kumeneko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anawasiya natuluka mu mzindawo ndi kupita ku Betaniya, kumene anakagona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anawasiya, naturuka m'mzinda, napita ku Betaniya, nagona kumeneko.