Matthew 21:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'maŵa mwake, m'mamaŵa ndithu, pamene Yesu ankabwerera ku Yerusalemu, adaamva njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mamawa, m'mene Iye analinkunkanso kumzinda, anamva njala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmamawa, pamene amabwera ku mzinda, anamva njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mamawa, m'mene Iye analinkunkanso kumzinda, anamva njala,