Matthew 21:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
naŵauza kuti, “Pitani m'mudzi mukuwonawo. Mukakangoloŵamo, mukapeza bulu ali chimangire, ndi mwana wake ali naye pamodzi. Mukaŵamasule nkubwera nawo kuno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena kwa iwo, Mukani kumudzi wopenyana ndi inu, ndipo pomwepo mudzapeza bulu womangidwa, ndi mwana wake pamodzi naye, masulani iwo, mudze nao kwa Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nawawuza kuti, “Pitani ku mudzi uli patsogolo panu, ndipo mukakangolowa mʼmenemo mukapeza bulu womangidwa ali ndi mwana pa mbali pake. Mukawamasule ndipo mubwere nawo kwa Ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena kwa iwo, Mukani ku mudzi wopenyana ndi inu, ndipo pomwepo mudzapeza buru womangidwa, ndi mwana wace pamodzi nave, masulani iwo, mudze nao kwa Ine.