Matthew 21:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ophunzira aja adaona zimenezi, adadabwa nafunsa Yesu kuti, “Mkuyuwu wauma bwanji nthaŵi yomweyi?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ophunzira poona ichi anazizwa, nati, Mkuyuwo unafota bwanji msanga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ophunzira ataona zimenezi, anadabwa nafunsa kuti, “Kodi mtengo wamkuyuwu wauma msanga bwanji?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ophunzira poona ici anazizwa, nati, Mkuyuwo unafota bwanji msanga?