Matthew 21:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma alimiwo adaŵagwira antchito aja, wina kummenya, wina kumupha, wina kumponya miyala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo olimawo anatenga akapolo ake, nampanda mmodzi, wina namupha, wina namponya miyala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Alimi aja anagwira antchito ake; namenya mmodzi, napha wina, ndi kumuponya miyala wachitatuyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo olimawo anatenga akapolo ace, nampanda mmodzi, wina namupha, wina namponya miyala.