Matthew 21:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potsiriza pake adaŵatumira mwana wake, nanena kuti, ‘Mwana wanga yekhayu akamchitira ulemu.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pambuyo pake anatumiza kwa iwo mwana wake, nati, Adzachitira mwana wanga ulemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pomalizira anatumiza mwana wake. Anati adzamuchitira ulemu mwana wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pambuyo pace anatumiza kwa iwo mwana wace, nati, Adzacitira mwana wanga ulemu.