Matthew 21:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adamugwiradi, namuponya kunja kwa mundawo, nkumupha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamtenga iye, namponya kunja kwa munda, namupha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo anamutenga namuponyera kunja kwa munda wamphesa namupha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamtenga iye, namponya kunja kwa munda, namupha.