Matthew 21:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kodi mwini munda wamphesa uja akadzafika, adzaŵatani alimi aja?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono atabwera mwini munda, adzachitira olimawo chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsono akabwera mwini munda wamphesa adzachita nawo chiyani matenantiwo?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono atabwera mwini munda, adzacitira olimawo ciani?