Matthew 21:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene akulu a ansembe ndi Afarisi adamva mafanizo ameneŵa a Yesu, adazindikira kuti ankanena iwowo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ansembe aakulu ndi Afarisi, pakumva mafanizo ake, anazindikira kuti alikunena za iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akulu a ansembe ndi Afarisi atamva mafanizo a Yesu, anadziwa kuti ankanena iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ansembe akuru ndi Afarisi, pakumva mafanizo ace, anazindikira kuti alikunena za iwo.