Matthew 21:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ophunzira aja adapitadi nakachita monga momwe Yesu adaaŵalamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ophunzirawo anamuka, nachita monga Yesu anawauza;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ophunzirawo anapita nachita monga Yesu anawalamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ophunzirawo anamuka, nacita monga Yesu anawauza;