Matthew 21:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ambiri ankayala zovala zao mu mseu, ndipo ena adakadula nthambi za mitengo nkumaziyalika mumseumo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ambirimbiri a mpingowo anayala zovala zao panjira; ndipo ena anadula nthambi za mitengo, naziyala m'njiramo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gulu lalikulu la anthu linayala zovala zawo mu msewu pamene ena anadula nthambi zamitengo ndi kuziyala mu msewumo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ambirimbiri a mpingowo anayala zobvala zao panjira; Ndipo ena anadula nthambi za mitengo, naziyala m'njirarno.