Matthew 22:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mmodzi mwa iwo, katswiri wa Malamulo, adafunsa Yesu funso kuti amutape m'kamwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mmodzi wa iwo, mphunzitsi wa chilamulo, anamfunsa ndi kumuyesa Iye, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmodzi wa iwo, katswiri wa malamulo anamuyesa Iye ndi funso ndipo anati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mmodzi wa iwo, mphunzitsi wa cilamulo, anamfunsa ndi kumuyesa Iye, nati,