Matthew 23:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakati panupa wamkulu akhale mtumiki wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma wamkulu wopambana wa inu adzakhala mtumiki wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wamkulu pakati panu adzakhala wokutumikirani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma wamkuru wopambana wa inu adzakhala mtumiki wanu.