Matthew 23:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Njoka inu, ana a mamba, mudzachipeŵa bwanji chilango cha ku Gehena?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Njoka inu, obadwa inu a mamba, mudzatha bwanji kuthawa kulanga kwake kwa Gehena?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Njoka inu! Ana amamba! Mudzachithawa bwanji chilango cha gehena?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Njoka inu, obadwa inu a mamba, mudzatha bwanji kuthawa kulanga kwace kwa gehena?