Matthew 23:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero chilango chidzakugwerani chifukwa cha anthu olungama onse amene adaphedwa, kuyambira kuphedwa kwa Abele, munthu wolungama uja, mpaka kuphedwa kwa Zakariya, mwana wa Barakiya, amene mudamuphera m'Nyumba ya Mulungu pakati pa guwa lansembe ndi Malo Opatulika kopambana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kotero kuti udzafika pa inu mwazi wonse wotayidwa pa dziko lapansi, kuyambira kumwazi wa Abele wolungamayo, kufikira kumwazi wa Zekariya mwana wa Barakiya, amene munamupha pakati pa Kachisi ndi guwa la nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo magazi onse a olungama amene anakhetsedwa pansi pano, kuyambira magazi a Abele, olungama kufikira Zakariya mwana wa Barakiya, amene munamupha pakati pa Nyumba ya Mulungu ndi guwa lansembe, adzakhala pa inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kotero kuti udzafika pa inu mwazi wonse wotayidwa pa dziko lapansi, kuyambira ku mwazi wa Abele wolungamayo, kufikira ku mwazi wa Zakariya mwana wa Barakiya, amene munamupha pakati pa Kacisi ndi guwa la nsembe.