Matthew 23:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amakondanso kuti anthu aziŵalonjera mwaulemu pa misika, ndipo kuti aziŵatchula aphunzitsi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kulonjeredwa m'misika, ndi kutchedwa ndi anthu, Rabi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amakondwera ndi kupatsidwa moni mʼmisika ndi kutchulidwa kuti ‘Aphunzitsi.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kulankhulidwa m'misika, ndi kuchedwa ndi anthu, Rabi.