Matthew 24:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono popeza kuti zoipa zizidzachulukirachulukira, chikondi chizidzacheperachepera pakati pa anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chifukwa cha kuchuluka kwa kusaweruzika, chikondano cha anthu aunyinji chidzazilala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha kuchuluka kwa zoyipa, chikondi cha ambiri chidzazirala,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cifukwa ca kucuruka kwa kusayeruzika, cikondano ca anthu aunyinji cidzazirala.