Matthew 24:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene ali padenga pa nyumba yake, asatsike nkuloŵanso m'nyumba mwake kuti akatenge katundu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iye ali pamwamba pa chindwi, asatsikire kunyamula za m'nyumba mwake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yemwe ali pa denga la nyumba yake asatsike kukatulutsa chinthu chilichonse mʼnyumba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iye ali pamwamba pa chindwi, asatsikire kunyamula za m'nyumba mwace;