Matthew 24:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pempherani kuti nthaŵi pamene muzidzathaŵa, isadzakhale nyengo yachisanu, kapena pa tsiku la Sabata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pempherani kuti kuthawa kwanu kusakhale pa nyengo yachisanu, kapena pa Sabata;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pempherani kuti kuthawa kwanu kusadzachitike nthawi yozizira kapena pa Sabata.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pempherani kuti kuthawa kwanu kusakhale pa nyengo yacisanu, kapena pa Sabata;