Matthew 24:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mvetsetsani, Ine ndiye ndakuuziranitu zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake akanena kwa inu, Onani, Iye ali m'chipululu; musamukeko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onani, ndakuwuzani izi nthawi isanafike.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace akanena kwa inu, Onani, Iye ali m'cipululu; musamukeko.