Matthew 24:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye adzayamba kumenya antchito anzake, ndiponso kumadya ndi kumamwa pamodzi ndi zidakwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nadzayamba kupanda akapolo anzake, nadya ndi kumwa pamodzi ndi oledzera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nayamba kumenya antchito anzake, nadya ndi kumwa ndi zidakwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nadzayamba kupanda akapolo anzace, nadya ndi kumwa pamodzi ndi oledzera;