Matthew 25:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomaliza Yesu adati, “Ndiyetu inu, muzikhala maso, poti simudziŵa tsiku lake kapena nthaŵi yake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake dikirani, pakuti simudziwa tsiku lake, kapena nthawi yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Choncho khalani odikira, popeza simudziwa tsiku kapena nthawi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace dikirani, pakuti simudziwa tsiku lace, kapena nthawi yace.