Matthew 25:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma amene adaalandira ndalama imodzi uja, adapita nakaikumbira pansi ndalama ya mbuye wake ija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma uyo amene analandira imodziyo anamuka, nakumba pansi, naibisa talente ya mbuye wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma munthu amene analandira 1,000 uja, anapita nakumba dzenje nabisapo ndalama ya mbuye wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma uyo amene analandira imodziyo anamuka, nakumba pansi, naibisa ndalama ya mbuye wace.