Matthew 25:43 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaali mlendo, inu osandilandira kunyumba kwanu. Ndidaali wamaliseche, inu osandiveka. Ndinkadwala, ndidaalinso m'ndende, inu osadzandichetsa.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndinali mlendo, ndipo simunandilandira Ine; wamaliseche ndipo simunandiveka Ine; wodwala, ndi m'nyumba yandende, ndipo simunadza kundiona Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndinali mlendo koma inu simunandilandire, ndinali wa usiwa koma simunandiveke, ndinali wodwala komanso ku ndende simunandisamalire.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndinali mlendo, ndipo simunandilandira Ine; wamarisece ndipo simunandibveka Ine; wodwala, ndi m'nyumba yandende, ndipo simunadza kundiona Ine.