Matthew 25:46 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo iwowo adzachoka kumapita ku chilango chosatha, olungama aja nkumapita ku moyo wosatha.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amenewa adzachoka kunka ku chilango cha nthawi zonse; koma olungama kumoyo wa nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Amenewa adzapita ku chilango chosatha pamene olungama ku moyo wosatha.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amenewa adzacoka kumka ku cilango ca nthawi zonse; koma olungama ku moyo wa nthawi zonse.