Matthew 25:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono pakati pa usiku kudamveka kufuula kuti, ‘Mkwati akubwera! Tulukani, kamchingamireni!’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pakati pa usiku panali kufuula, Onani, mkwati! Tulukani kukakomana naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pakati pa usiku kunamveka kufuwula kuti, ‘Onani Mkwati! Tulukani kuti mukakumane naye!’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pakati pa usiku panali kupfuula, Onani, mkwati! turukani kukakomana naye.