Matthew 26:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kutada, Yesu ndi ophunzira ake khumi ndi aŵiri aja adakhala pamodzi nkumadya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakufika madzulo, Iye analinkukhala pachakudya pamodzi ndi ophunzira khumi ndi awiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kutada, Yesu ndi ophunzira ake khumi ndi awiriwo anakhala pa tebulo nʼkumadya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakufika madzulo, Iye analikukhala pacakudya pamodzi ndi ophunzira khumi ndi awiri;