Matthew 26:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ophunzirawo adamva chisoni kwambiri, nayamba mmodzimmodzi kumufunsa kuti, “Monga nkukhala ine, Ambuye?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo anagwidwa ndi chisoni chachikulu, nayamba kunena kwa Iye mmodzimmodzi, Kodi ndine, Ambuye?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anamva chisoni kwambiri ndipo anayamba kuyankhulana naye mmodzimmodzi nati, “Kodi nʼkukhala ine Ambuye?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo anagwidwa ndi cisoni cacikuru, nayamba kunena kwa Iye mmodzi mmodzi, Kodi ndine, Ambuye?