Matthew 26:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adatenga chikho, nathokoza Mulungu nkuchipereka kwa ophunzirawo. Adaŵauza kuti, “Imwani nonsenu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anatenga chikho, anayamika, napatsa iwo, nanena, Mumwere ichi inu nonse,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anatenga chikho, nayamika nachipereka kwa iwo nati, “Imwani nonsenu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anatenga cikho, anayamika, napatsa iwo, nanena, Mumwere ici inu nonse,