Matthew 26:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatengako Petro ndi ana aŵiri aja a Zebedeo. Yesu adayamba kugwidwa ndi chisoni ndi kuvutika mu mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatenga Petro ndi ana awiri a Zebedeo pamodzi naye, nayamba kugwidwa ndi chisoni ndi kuthedwa nzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anatenga Petro ndi ana awiri a Zebedayo, ndipo anayamba kumva chisoni ndi kuvutika mu mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatenga Petro ndi ana awiria Zebedayo pamodzi naye, nayamba kugwidwa ndi cisoni ndi kuthedwa nzeru.