Matthew 26:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ankati, “Zimenezi tisadzachite pa nthaŵi ya chikondwerero ai, pangadzachitike chipolowe pakati pa anthu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ananena iwo, pa nthawi la chikondwerero iai, kuti pasakhale phokoso la anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anati, “Osati nthawi yaphwando chifukwa pangabuke chipolowe pakati pa anthu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ananena iwo, Pa dzuwa la cakudya iai, kuti pasakhale phokoso la anthu.