Matthew 26:54 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndikadatero, nanga zikadachitika bwanji zimene Malembo adaneneratu kuti ziyenera kuchitika?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pakutero malembo adzakwaniridwa bwanji, pakuti kuyenera chomwecho?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nanga malemba akwaniritsidwa bwanji amene akuti ziyenera kuchitika motere?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pakutero malembo adzakwaniridwa bwanji, pakuti kuyenera comweco?