Matthew 26:60 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma sadaupeze ngakhale padaabwera mboni zambiri zabodza. Potsiriza padabwera anthu aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma sanaupeze zingakhale mboni zonama zambiri zinadza. Koma pambuyo pake anadza awiri,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma sanathe kupeza uliwonse, angakhale kuti mboni zambiri zabodza zinapezeka. Pomalizira mboni ziwiri zinabwera patsogolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma sanaupeza zingakhale 2 mboni zonama zambiri zinadza. Koma pambuyo pace anadza awiri,