Matthew 26:66 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye inu mukuganiza bwanji?” Iwo aja adayankha kuti, “Ayenera kuphedwa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
muganiza bwanji? Iwo anayankha nati, Ali woyenera kumupha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukuganiza bwanji?” Iwo anayankha kuti, “Ayenera kuphedwa!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
muganiza bwanji? lwo anayankha nati, 7 Ali woyenera kumupha,