Matthew 26:67 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo iwo adayamba kumthira malovu kumaso nkumamumenya, ena kumamuwomba makofi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomwepo iwo anathira malovu pankhope pake, nambwanyula Iye; ndipo ena anampanda khofu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anamulavulira kumaso namumenya ndi zibakera. Ena anamumenya makofi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
8 Pomwepo iwo anathira malobvu pankhope pace, nambwanyula Iye; ndipo ena anampanda kofu,