Matthew 26:68 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nkumanena kuti, “Iwe Mpulumutsi wolonjezedwa uja, nanga sindiwe mneneri? Lota, wakumenya ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati, Utilote ife, Khristu Iwe; wakumenya Iwe ndani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anati, “Tanenera kwa ife, Khristu. Wakumenya ndani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati, 9 Utilote ife, Kristu Iwe; wakumenya Iwe ndani?