Matthew 26:70 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma iye adakana pamaso pa anthu onse, adati, “Sindikuzidziŵa zimenezo ine.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye anakana pamaso pa anthu onse, kuti, Chimene unena sindichidziwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma iye anakana pamaso pawo nati, “Sindikudziwa chimene ukunena.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye anakana pamaso pa anthu onse, kuti, Cimene unena sindicidziwa.