Matthew 26:72 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Petro adakananso molumbira kuti, “Ndithudi sindikumdziŵa munthu ameneyo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakananso ndi chilumbiro, kuti, Sindidziwa munthuyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakananso molumbira kuti, “Sindimudziwa munthuyu!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakananso ndi cilumbiro, kuti, Sindidziwa munthuyo.