Matthew 27:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nagulira munda wa mmisiri wa mbiya, monga momwe Ambuye adaandilamulira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anazipereka kugula munda wa woumba mbiya, monga anandilamulira ine Ambuye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anazigwiritsa ntchito kugula munda wa wowumba mbiya monga mmene Ambuye anandilamulira ine.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anazipereka kugula munda wa woumba mbiya, Monga anandilamulira ine Ambuye.