Matthew 27:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pamene akulu a ansembe ndi akulu a Ayuda aja ankamuneneza, Yesu sadayankhepo kanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakumnenera Iye ansembe aakulu ndi akulu, Iye sanayankhe kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene akulu a ansembe ndi akuluakulu ankamuneneza, sanayankhe kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakumnenera Iye ansembe akuru ndi akuru, Iye sanayankha kanthu.