Matthew 27:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi imeneyo panali mkaidi wina wodziŵika, dzina lake Barabasi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pa nthawi yomweyo anali ndi wandende wodziwika, dzina lake Barabasi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawiyo anali ndi wamʼndende woyipa kwambiri dzina lake Baraba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pa nthawi yomweyo anali ndi wandende wodziwika, dzina lace Baraba.