Matthew 27:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse aja adati, “Imfayo mlandu wake ugwere ife ndi ana athu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse anavomereza, ndi kuti, Mwazi wake uli pa ife ndi pa ana athu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse anayankha nati, “Magazi ake akhale pa ife ndi pa ana athu!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse anabvomereza, ndi kuti, Mwazi wace uli pa ife ndi pa ana athu.