Matthew 27:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamuvula zovala zake, namuveka chovala chofiira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anavula malaya ake, namveka malaya ofiira achifumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anamuvula malaya ake namuveka Iye malaya ofiira aufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anabvula malaya ace, nambveka malaya ofiira acifumu.