Matthew 27:56 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakati pao panali Maria wa ku Magadala, Maria mai wa Yakobe ndi Yosefe, ndiponso mai wa ana a Zebedeo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mwa iwo amene munali Maria wa Magadala, ndi Maria amake wa Yakobo, ndi wa Yosefe, ndi amake wa ana a Zebedeo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakati pawo panali Mariya wa ku Magadala, Mariya amayi ake Yakobo ndi Yosefe ndi amayi a ana a Zebedayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mwa iwo 13 amene munali Mariya wa Magadala, ndi Mariya amace wa Yakobo, ndi wa Yose, ndi amace wa ana a Zebedayo.