Matthew 27:61 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maria wa ku Magadala ndi Maria wina uja anali pomwepo atakhala pansi kuyang'anana ndi mandawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Maria wa Magadala anali pamenepo, ndi Maria winayo, anakhala pansi popenyana ndi mandawo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mariya wa Magadala ndi Mariya wina anakhala pansi moyangʼanizana ndi mandawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mariya wa Magadala anali pamenepo, ndi Mariya winayo, anakhala pansi popenyana ndi mandawoo