Matthew 27:63 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamuuza kuti, “Bwana, tikukumbukira kuti munthu wonyenga uja akali moyo ankati, ‘Patapita masiku atatu, ndidzaukanso.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena, Mfumu, takumbukira ife kuti wonyenga uja anati, pamene anali ndi moyo, Ndidzauka pofika masiku atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati, “Bwana takumbukira kuti munthu wonyenga uja akanali ndi moyo anati, ‘Pakatha masiku atatu ndidzauka.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena, Mfumu, takumbukira ife kuti wonyenga uja anati, pamene anali ndi moyo, 15 Ndidzaukapofikamasikuatatu.