Matthew 27:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake mpaka lero mundawo umatchedwa “Munda wa Magazi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake munda umenewu anautcha, Munda-wa-mwazi, kufikira lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi chifukwa chake umatchedwa munda wamagazi mpaka lero lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace munda umenewu anaucha, Munda-wa-mwazi, kufikira lero lino.