Matthew 27:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero zidapherezera zimene mneneri Yeremiya adaanena kuti, “Adatenga ndalama zija makumi atatu, mtengo wake umene Aisraele adaagamula,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo chinakwaniridwa chonenedwa ndi Yeremiya mneneri, ndi kuti, Ndipo iwo anatenga ndalamazo zasiliva makumi atatu, mtengo wa uja wowerengedwa mtengo wake, amene iwo a ana a Israele anawerenga mtengo wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo zimene anayankhula mneneri Yeremiya zinakwaniritsidwa kuti, “Anatenga ndalama zamasiliva makumi atatu mtengo umene anamuyikira Iye anthu a Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo cinakwaniridwa conenedwa ndi Yeremiya mneneri, ndi kuti, Ndipo iwo anatenga ndalamazo zasiliva makumi atatu, Mtengo wa uja wowerengedwa mtengo wace, Amene iwo a ana a Israyeli anawerenga mtengo wace;