Matthew 28:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo alonda aja adachita mantha nayamba kunjenjemera, nkungoti gwa ngati anthu akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndi kuopsa kwake alondawo ananthunthumira, nakhala ngati anthu akufa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Alondawo anachita naye mantha kwambiri kotero kuti ananjenjemera ndi kuwuma ngati akufa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndi kuopsa kwace alondawo ananthunthumira, nakhala ngati anthu akufa.