Matthew 3:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankati, “Tembenukani mtima chifukwa Mulungu ali pafupi kukhazikitsa ufumu wake tsopano.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena, Tembenukani mitima; chifukwa Ufumu wa Kumwamba wayandikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti, “Tembenukani mtima chifukwa ufumu wakumwamba wayandikira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena, Tembenukani mitima; cifukwa Ufumu wa Kumwamba wayandikira.